Skip to content Skip to sidebar Skip to footer

(DOWNLOAD) "Mtengo Ndi Utumiki Wanu" by Dag Heward-Mills " eBook PDF Kindle ePub Free

Mtengo Ndi Utumiki Wanu

📘 Read Now     📥 Download


eBook details

  • Title: Mtengo Ndi Utumiki Wanu
  • Author : Dag Heward-Mills
  • Release Date : January 22, 2019
  • Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
  • Pages : * pages
  • Size : 495 KB

Description

Anthu ambiri samamvetsetsa za malo a mtengo wa dzindikila chabwino ndi choipa m`moyo mwathu. Nthawi zambiri timaganiza kuti unali mtengo qmwe unalipo kalekale munthawi ya Adamu ndi Eva. Timakhulupirira kuti mtengo umeneyo unali ndi zipatso za poizoni zoti ukangodya yemwe wadyayo amafa.
Mwa tsoka, Adamu ndi Eva anadya za mtengowu ndipo anafa. Tikawerenga za nkhaniyi, timaganiza kwa ife, “zinali zomvetsa chisoni Adam ndi Eva kudya chipatso chakuphachi koma tithokoze sitidzaikidwa m`mayeselo ndi mtengo ngati umenewo”.
Zachisoni, tikhala tikulimbana ndi mtengo umenewu ndi zipatso zake. Chomwe tiyenera kudziwa ndi chakuti za mtengo wa kudzindikira chabwino ndi choipa udakalipobe mpaka lero. Umagwira ntchito m`mayesero kwa ife chimodzimodzi m`mene unapangira nthawi ya Adamu ndi Eva. Umayimilira ngati njira ina ya kwa Mulungu


Books Free Download "Mtengo Ndi Utumiki Wanu" PDF ePub Kindle